Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




2 Mafumu 11:8 - Buku Lopatulika

8 Ndipo muzizinga mfumu, yense zida zake m'manja mwake, ndi iye wakulowa poima inupo aphedwe; ndipo muzikhala inu ndi mfumu potuluka ndi polowa iye.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

8 Ndipo muzizinga mfumu, yense zida zake m'manja mwake, ndi iye wakulowa poima inupo aphedwe; ndipo muzikhala inu ndi mfumu potuluka ndi polowa iye.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

8 Mudzazungulire mfumuyo, aliyense atatenga zida m'manja. Wina aliyense amene at ayandikire pafupi, aphedwe. Muzikhala nayo mfumu kulikonse kumene iziyenda.”

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

8 Mudzakhale mozungulira mfumuyo, munthu aliyense ali ndi chida mʼmanja mwake. Wina aliyense amene adzakuyandikireni adzayenera kuphedwa. Muzikhala pafupi ndi mfumu kulikonse kumene ikupita.”

Onani mutuwo Koperani




2 Mafumu 11:8
7 Mawu Ofanana  

Koma Yehoyada wansembe analamulira atsogoleri a mazana oyang'anira khamu, nanena nao, Mumtulutse mkaziyo pabwalo pakati pa mipambo; womtsata iye mumuphe ndi lupanga; pakuti wansembe adati, Asaphedwe m'nyumba ya Yehova.


Ndipo magawo awiri a inu, ndiwo onse otulukira pa Sabata, azilindira nyumba ya Yehova kuzinga mfumu.


Ndipo Alevi amzinge mfumu pozungulirapo, yense ndi zida zake m'dzanja mwake; ndipo aliyense wolowa m'nyumba aphedwe; nimukhale inu pamodzi ndi mfumu pakulowa ndi pakutuluka iye.


Koma munthu akachita dala pa mnzake, kumupha monyenga; uzimchotsa ku guwa langa la nsembe, kuti afe.


Yehova, Mulungu wa mizimu ya anthu onse, aike munthu pa khamulo,


wakutuluka pamaso pao, ndi kulowa pamaso pao, wakuwatulutsa ndi kuwalowetsa; kuti khamu la Yehova lisakhale ngati nkhosa zopanda mbusa.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa