Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




2 Mafumu 11:7 - Buku Lopatulika

7 Ndipo magawo awiri a inu, ndiwo onse otulukira pa Sabata, azilindira nyumba ya Yehova kuzinga mfumu.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

7 Ndipo magawo awiri a inu, ndiwo onse otulukira pa Sabata, azilindira nyumba ya Yehova kuzinga mfumu.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

7 Tsono enawo a m'zigawo ziŵiri zija odzaŵeruka ntchito pa Sabata, iwo adzalonde ku Nyumba ya Chauta, kuti aziteteza mfumu.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

7 Ndipo inu amene muli mʼmagulu ena awiri amene simugwira ntchito pa tsiku la Sabata, nonse mudzalondere mfumu ku nyumbayo.

Onani mutuwo Koperani




2 Mafumu 11:7
5 Mawu Ofanana  

Nawalamulira, kuti, Chochita inu ndi ichi: limodzi la magawo atatu la inu olowa pa Sabata lizilindira nyumba ya mfumu,


ndi lina lizikhala ku chipata cha Suri, ndi lina ku chipata kumbuyo kwa otumikira; momwemo muzisunga nyumba, ndi kuitchinjiriza.


Ndipo muzizinga mfumu, yense zida zake m'manja mwake, ndi iye wakulowa poima inupo aphedwe; ndipo muzikhala inu ndi mfumu potuluka ndi polowa iye.


Ndi abale ao m'midzi mwao akafikafika, atapita masiku asanu ndi awiri masabata onse, kuti akhale nao;


Koma asalowe mmodzi m'nyumba ya Yehova, ansembe okha, ndi Alevi otumikira, alowe iwowa; pakuti ndiwo opatulika; koma anthu onse asunge udikiro wa Yehova.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa