2 Mafumu 11:3 - Buku Lopatulika3 Nakhala naye wobisika m'nyumba ya Yehova zaka zisanu ndi chimodzi; ndipo Ataliya anakhala mfumu ya dziko. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20143 Nakhala naye wobisika m'nyumba ya Yehova zaka zisanu ndi chimodzi; ndipo Ataliya anakhala mfumu ya dziko. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa3 Mwanayo adakhala ndi mlezi wake zaka zisanu ndi chimodzi akubisala m'Nyumba ya Chauta, pamene Ataliya ankalamulira dzikolo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero3 Mwanayo anakhala mobisala pamodzi ndi mlezi wake mʼnyumba ya Yehova kwa zaka zisanu ndi chimodzi pamene Ataliya ankalamulira dzikolo. Onani mutuwo |