Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




2 Mafumu 11:21 - Buku Lopatulika

21 Yowasi anali wa zaka zisanu ndi ziwiri polowa iye ufumu.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

21 Yowasi anali wa zaka zisanu ndi ziwiri polowa iye ufumu.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

21 Yowasiyo anali wa zaka zisanu ndi ziŵiri pamene adaloŵa ufumu.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

21 Yowasi anali wa zaka zisanu ndi ziwiri pamene anayamba kulamulira.

Onani mutuwo Koperani




2 Mafumu 11:21
5 Mawu Ofanana  

Koma Yehoseba mwana wa mfumu Yoramu, mlongo wake wa Ahaziya, anatenga Yowasi mwana wa Ahaziya, namuba pakati pa ana a mfumu akuti aphedwe, iye ndi mlezi, nawaika m'chipinda chogonamo; nambisira Ataliya, ndipo sanaphedwe.


Koma chaka chachisanu ndi chiwiri Yehoyada anaitanitsa atsogoleri a mazana a opha anthu, ndi a otumikira, nabwera nao kwa iye kunyumba ya Yehova, napangana nao, nawalumbiritsa m'nyumba ya Yehova, nawaonetsa mwana wa mfumu.


Chaka chachisanu ndi chiwiri cha Yehu, Yowasi analowa ufumu wake; nakhala mfumu mu Yerusalemu zaka makumi anai; ndi dzina la mai wake ndiye Zibiya wa ku Beereseba.


Yosiya ndiye wa zaka zisanu ndi zitatu polowa ufumu wake, nakhala mfumu zaka makumi atatu mphambu chimodzi mu Yerusalemu; ndi dzina la make ndi Yedida mwana wa Adaya wa ku Bozikati.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa