2 Mafumu 11:16 - Buku Lopatulika16 Ndipo anamgwira, napita naye njira yolowera akavalo kunyumba ya mfumu, namupha pomwepo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201416 Ndipo anamgwira, napita naye njira yolowera akavalo kunyumba ya mfumu, namupha pomwepo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa16 Choncho anthuwo adamgwira Ataliya uja, ndipo atafika naye ku nyumba ya mfumu, pakhomo lotchedwa la Akavalo, adamuphera pamenepo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero16 Choncho anamugwira pamene amafika pa malo amene akavalo amalowera ku nyumba ya mfumu ndipo anamuphera pamenepo. Onani mutuwo |