2 Mafumu 11:13 - Buku Lopatulika13 Pamene Ataliya anamva phokoso la otumikira ndi anthu, anadza kwa anthu m'nyumba ya Yehova; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201413 Pamene Ataliya anamva phokoso la otumikira ndi anthu, anadza kwa anthu m'nyumba ya Yehova; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa13 Tsono mfumukazi Ataliya, atamva phokoso la asilikali ndi la anthu, adapita ku Nyumba ya Chauta. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero13 Ataliya atamva phokoso limene alonda ndi anthuwo amachita, anapita ku Nyumba ya Yehova kumene kunali anthuwo. Onani mutuwo |