2 Mafumu 10:4 - Buku Lopatulika4 Koma anaopa kwambiri, nati, Taonani, mafumu awiri sanaime pamaso pake, nanga ife tidzaima bwanji? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20144 Koma anaopa kwambiri, nati, Taonani, mafumu awiri sanaime pamaso pake, nanga ife tidzaima bwanji? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa4 Koma anthuwo adachita mantha kwambiri, ndipo adati, “Ha! Mafumu aŵiri aja sadathe kulimbana naye Yehu, nanga ife ndiye tingathe bwanji?” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero4 Koma anthuwo anachita mantha kwambiri ndipo anati, “Taonani, mafumu awiri sanathe kulimbana naye, nanga ife tingathe bwanji?” Onani mutuwo |