2 Mafumu 10:36 - Buku Lopatulika36 Ndipo masiku ake akukhala Yehu mfumu ya Israele mu Samariya ndiwo zaka makumi awiri mphambu zisanu ndi zitatu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201436 Ndipo masiku ake akukhala Yehu mfumu ya Israele m'Samariya ndiwo zaka makumi awiri mphambu zisanu ndi zitatu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa36 Yehu adalamulira Aisraele ku Samariya zaka 28. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero36 Yehu analamulira Aisraeli ku Samariya zaka 28. Onani mutuwo |