2 Mafumu 10:34 - Buku Lopatulika34 Ndipo machitidwe ena a Yehu, ndi zonse anazichita, ndi mphambu yake yonse, sizinalembedwe kodi m'buku la machitidwe a mafumu a Israele? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201434 Ndipo machitidwe ena a Yehu, ndi zonse anazichita, ndi mphambu yake yonse, sizinalembedwa kodi m'buku la machitidwe a mafumu a Israele? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa34 Tsono ntchito zina za Yehu ndi zonse zimene adazichita, zidalembedwa m'buku la Mbiri ya Mafumu a ku Israele. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero34 Ntchito zina za Yehu ndi zonse zimene anachita, kodi sizinalembedwe mʼbuku la mbiri ya mafumu a ku Israeli? Onani mutuwo |