2 Mafumu 10:24 - Buku Lopatulika24 Nalowa iwo kupereka nsembe zophera ndi nsembe zopsereza. Koma Yehu adadziikira kubwalo amuna makumi asanu ndi atatu, nati, Munthu akalola wina wa anthuwa ndilikuwaika m'manja mwanu apulumuke, moyo wake kulipa moyo wake. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201424 Nalowa iwo kupereka nsembe zophera ndi nsembe zopsereza. Koma Yehu adadziikira kubwalo amuna makumi asanu ndi atatu, nati, Munthu akalola wina wa anthuwa ndilikuwaika m'manja mwanu apulumuke, moyo wake kulipa moyo wake. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa24 Tsono Yehu adaloŵa kukapereka nsembe zopsereza. Koma Yehu anali ataika anthu 80 panja naŵauza kuti, “Adzaphedwa amene athaŵitse aliyense mwa anthu amene ndikupatseni kuti muŵapheŵa.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero24 Choncho Yehu analowa kukapereka nsembe zina ndi nsembe zopsereza. Nthawi iyi nʼkuti Yehu atayika anthu 80 kunja kwa nyumbayo ndi chenjezo lakuti, “Ngati wina aliyense wa inu adzathawitsa wina aliyense wa anthu amene ndayika kuti muziwayangʼanira, munthu woteroyo adzaphedwa.” Onani mutuwo |