Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




2 Mafumu 10:22 - Buku Lopatulika

22 Nati kwa iye wosunga nyumba ya zovala, Tulutsira otumikira Baala onse zovala. Nawatulutsira zovala.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

22 Nati kwa iye wosunga nyumba ya zovala, Tulutsira otumikira Baala onse zovala. Nawatulutsira zovala.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

22 Tsono Yehu adauza munthu wosunga zovala kuti, “Bwera ndi zovala zopatulika zokwanira anthu onse opembedza Baala.” Munthuyo adaŵatengera zovalazo anthu aja.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

22 Ndipo Yehu anawuza munthu wosunga mikanjo kuti, “Bweretsa mikanjo yokwanira atumiki onse a Baala.” Ndipo iye anabweretsa mikanjoyo.

Onani mutuwo Koperani




2 Mafumu 10:22
4 Mawu Ofanana  

Ndipo Yehu anatumiza kwa Aisraele onse, nadza otumikira Baala onse, wosatsala ndi mmodzi yense wosafika. Nalowa m'nyumba ya Baala; ndi nyumba ya Baala inadzala phaa.


Nalowa Yehu ndi Yehonadabu mwana wa Rekabu m'nyumba ya Baala, nati kwa otumikira Baala, Mufunefune, nimuone asakhale nanu muno otumikira Yehova, koma otumikira Baala okha.


Ndipo usokere Aroni mbale wako zovala zopatulika, zikhale zaulemerero ndi zokoma.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa