Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




2 Mafumu 10:12 - Buku Lopatulika

12 Pamenepo ananyamuka, nachoka, namuka ku Samariya. Ndipo pokhala kunyumba yosengera ya abusa panjira,

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

12 Pamenepo ananyamuka, nachoka, namuka ku Samariya. Ndipo pokhala kunyumba yosengera ya abusa panjira,

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

12 Pambuyo pake Yehu adanyamuka napita ku Samariya. Atafika pa malo otchedwa “Pogona abusa,”

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

12 Kenaka Yehu ananyamuka kupita ku Samariya. Atafika pa malo otchedwa Beti-Ekedi wa abusa,

Onani mutuwo Koperani




2 Mafumu 10:12
4 Mawu Ofanana  

Nawakantha Yehu otsala onse a nyumba ya Ahabu mu Yezireele, ndi omveka ake onse, ndi odziwana naye, ndi ansembe ake, mpaka sanatsale wa iye ndi mmodzi yense.


Yehu anakomana nao abale a Ahaziya mfumu ya Yuda, nati, Ndinu ayani? Nati iwo, Ife ndife abale a Ahaziya, tilikutsika kulonjera ana a mfumu, ndi ana a nyumba yaikulu.


Nati iye, Agwireni amoyo. Nawagwira amoyo, nawapha ku dzenje la nyumba yosengera, ndiwo amuna makumi anai mphambu awiri; sanasiye ndi mmodzi yense.


Ndipo kunali, pakulanga Yehu nyumba ya Ahabu, anapeza akalonga a Yuda, ndi ana a abale a Ahaziya, akutumikira Ahaziya, nawapha.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa