2 Mafumu 1:18 - Buku Lopatulika18 Machitidwe ake ena tsono adawachita Ahaziya, sanalembedwe kodi m'buku la machitidwe a mafumu a Israele? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201418 Machitidwe ake ena tsono adawachita Ahaziya, sanalembedwa kodi m'buku la machitidwe a mafumu a Israele? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa18 Tsono ntchito zina za Ahaziya pamodzi ndi zonse zimene adazichita zidalembedwa m'buku la Mbiri ya Mafumu a Aisraele. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero18 Ntchito zina zonse zimene Ahaziya anachita, kodi sizinalembedwe mʼbuku la mbiri ya mafumu a ku Israeli? Onani mutuwo |