2 Akorinto 9:9 - Buku Lopatulika9 monga kwalembedwa, Anabalalitsa, anapatsa kwa osauka; chilungamo chake chikhale kunthawi yonse. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20149 monga kwalembedwa, Anabalalitsa, anapatsa kwa osauka; chilungamo chake chikhale kunthawi yonse. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa9 Za munthu wotere paja Malembo akuti, “Wapereka mphatso zake moolowa manja kwa anthu osauka. Chilungamo chake nchamuyaya.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero9 Paja analemba kuti, “Wopereka mphatso zake mowolowamanja kwa osauka, chilungamo chake chimanka mpaka muyaya.” Onani mutuwo |