1 Yohane 4:21 - Buku Lopatulika21 Ndipo lamulo ili tili nalo lochokera kwa Iye, kuti iye amene akonda Mulungu akondenso mbale wake. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201421 Ndipo lamulo ili tili nalo lochokera kwa Iye, kuti iye amene akonda Mulungu akondenso mbale wake. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa21 Lamulo limene Iye adatipatsa ndi lakuti, wokonda Mulungu azikondanso mbale wake. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero21 Ndipo Iye anatipatsa lamulo lakuti: Aliyense amene amakonda Mulungu ayenera kukondanso mʼbale wake. Onani mutuwo |