Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




1 Yohane 4:13 - Buku Lopatulika

13 m'menemo tizindikira kuti tikhala mwa Iye, ndi Iye mwa ife, chifukwa anatipatsako Mzimu wake.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

13 m'menemo tizindikira kuti tikhala mwa Iye, ndi Iye mwa ife, chifukwa anatipatsako Mzimu wake.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

13 Tikudziŵa kuti timakhala mwa Mulungu, ndipo Iyenso amakhala mwa ife, chifukwa adatipatsa Mzimu wake Woyera.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

13 Ife tikudziwa kuti timakhala mwa Iye ndipo Iyeyo amakhala mwa ife chifukwa anatipatsa Mzimu wake.

Onani mutuwo Koperani




1 Yohane 4:13
11 Mawu Ofanana  

Koma sitinalandira ife mzimu wa dziko lapansi, koma Mzimu wa kwa Mulungu, kuti tikadziwe zimene zipatsidwa kwa ife ndi Mulungu kwaufulu.


Kapena simudziwa kuti thupi lanu lili Kachisi wa Mzimu Woyera, amene ali mwa inu, amene muli naye kwa Mulungu? Ndipo simukhala a inu nokha.


Ndipo umo tizindikira kuti tamzindikira Iye, ngati tisunga malamulo ake.


koma iye amene akasunga mau ake, mwa iyeyu zedi chikondi cha Mulungu chathedwa. M'menemo tizindikira kuti tili mwa Iye;


Ndipo munthu amene asunga malamulo ake akhala mwa Iye, ndi Iye mwa munthuyo. Ndipo m'menemo tizindikira kuti akhala mwa ife, kuchokera mwa Mzimu amene anatipatsa ife.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa