1 Yohane 2:6 - Buku Lopatulika6 iye wakunena kuti akhala mwa Iye, ayeneranso mwini wake kuyenda monga anayenda Iyeyo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20146 iye wakunena kuti akhala mwa Iye, ayeneranso mwini wake kuyenda monga anayenda Iyeyo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa6 Munthu akamati amakhala mwa Mulungu, zochita zake zizilingana ndi zimene Yesu ankachita. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero6 Aliyense amene amati amakhala mwa Mulungu, ayenera kukhala moyo umene Yesu ankakhala. Onani mutuwo |