1 Yohane 2:12 - Buku Lopatulika12 Ndikulemberani, tiana, popeza machimo adakhululukidwa kwa inu mwa dzina lake. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201412 Ndikulemberani, tiana, popeza machimo adakhululukidwa kwa inu mwa dzina lake. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa12 Inu ana, ndikukulemberani popeza kuti Mulungu wakukhululukirani machimo anu chifukwa cha dzina la Khristu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero12 Inu ana okondedwa, ndikukulemberani popeza kuti machimo anu akhululukidwa chifukwa cha dzina la Yesu. Onani mutuwo |