1 Timoteyo 5:9 - Buku Lopatulika9 Asawerengedwe wamasiye ngati sanafikire zaka makumi asanu ndi limodzi, atakhala mkazi wa mwamuna mmodzi, Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20149 Asawerengedwe wamasiye ngati sanafikire zaka makumi asanu ndi limodzi, atakhala mkazi wa mwamuna mmodzi, Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa9 Wina aliyense asaloledwe kuloŵa m'gulu la azimai amasiye, asanakwanitse zaka 60. Akhale woti adakwatiwapo ndi mwamuna mmodzi yekha. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero9 Mayi wamasiye aliyense amene sanakwanitse zaka 60 zakubadwa, asakhale mʼgulu la akazi amasiye. Akhale woti anakwatiwapo ndi mwamuna wake mmodzi yekha. Onani mutuwo |