1 Timoteyo 4:9 - Buku Lopatulika9 Okhulupirika mauwa ndi oyenera kulandiridwa konse. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20149 Okhulupirika mauwa ndi oyenera kulandiridwa konse. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa9 Ameneŵa ndi mau otsimikizika oyenera kuŵavomereza ndi mtima wonse. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero9 Amenewa ndi mawu odalirika ndi oyenera kuwalandira kwathunthu. Onani mutuwo |