1 Timoteyo 3:9 - Buku Lopatulika9 okhala nacho chinsinsi cha chikhulupiriro m'chikumbu mtima choona. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20149 okhala nacho chinsinsi cha chikhulupiriro m'chikumbu mtima choona. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa9 Akhale anthu a mtima wopanda kanthu koutsutsa posunga zoona za chikhulupiriro zimene Mulungu adaulula. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero9 Ayenera kugwiritsa mozama choonadi cha chikhulupiriro ndi kukhala ndi chikumbumtima chabwino. Onani mutuwo |