1 Timoteyo 3:12 - Buku Lopatulika12 Atumiki akhale mwamuna wa mkazi mmodzi, akuweruza bwino ana ao, ndi iwo a m'nyumba yao ya iwo okha. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201412 Atumiki akhale mwamuna wa mkazi mmodzi, akuweruza bwino ana ao, ndi iwo a m'nyumba yao ya iwo okha. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa12 Atumiki a mpingo akhale a mkazi mmodzi yekha. Akhale olera ana ao bwino, oyendetsanso bwino mabanja ao. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero12 Mtumiki akhale wokhulupirika kwa mkazi wake ndipo ayenera kukhala wosamalira bwino ana ake ndi onse a pa khomo pake. Onani mutuwo |