1 Timoteyo 3:10 - Buku Lopatulika10 Koma iwonso ayamba ayesedwe; pamenepo atumikire, akakhala opanda chifukwa. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201410 Koma iwonso ayamba ayesedwe; pamenepo atumikire, akakhala opanda chifukwa. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa10 Iwonso ayambe ayesedwa, ndipo pambuyo pake, ngati alibe chokayikitsa, ndiye asenze udindo wa atumiki. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero10 Ayambe ayesedwa kaye, ndipo ngati palibe kanthu kowatsutsa, aloleni akhale atumiki. Onani mutuwo |