1 Timoteyo 3:1 - Buku Lopatulika1 Mauwa ali okhulupirika, ngati munthu akhumba udindo wa woyang'anira, aifuna ntchito yabwino. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20141 Mauwa ali okhulupirika, ngati munthu akhumba udindo wa woyang'anira, aifuna ntchito yabwino. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa1 Aŵa ndi mau otsimikizika ndithu akuti, “Ngati munthu afuna ntchito ya kuyang'anira Mpingo, akukhumba ntchito yaulemu.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero1 Mawu woona ndi awa: Ngati munthu akufunitsitsa atakhala woyangʼanira, ndiye kuti akufuna ntchito yabwino. Onani mutuwo |