1 Timoteyo 2:12 - Buku Lopatulika12 Koma sindilola ine kuti mkazi aphunzitse, kapena kulamulira mwamuna; komatu akhale chete. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201412 Koma sindilola ine kuti mkazi aphunzitse, kapena kulamulira mwamuna; komatu akhale chete. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa12 Sindilola kuti mkazi aziphunzitsa kapena kukhala ndi ulamuliro pa amuna. Mkazi kwake nkukhala chete. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero12 Ine sindikulola kuti amayi aziphunzitsa kapena kulamulira amuna; koma akhale chete. Onani mutuwo |