Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




1 Timoteyo 2:11 - Buku Lopatulika

11 Mkazi aphunzire akhale wachete m'kumvera konse.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

11 Mkazi aphunzire akhale wachete m'kumvera konse.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

11 Akazi pophunzitsidwa, azikhala chete ndi a mtima wodzichepetsa.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

11 Amayi azikhala chete pophunzitsidwa ndi mtima ogonjera kwathunthu.

Onani mutuwo Koperani




1 Timoteyo 2:11
10 Mawu Ofanana  

Kwa mkaziyo ndipo anati, Ndidzachulukitsa kusauka kwako ndi potenga mimba pako; udzasauka pakubala: udzakhumba mwamuna wako, ndipo iye adzakulamulira iwe.


Ndipo mau amene adzaika mfumu akamveka mu ufumu wake wonse, (pakuti ndiwo waukulu), akazi onse adzachitira amuna ao ulemu, aakulu ndi aang'ono.


Koma ndifuna kuti mudziwe, kuti mutu wa munthu yense ndiye Khristu; ndi mutu wa mkazi ndiye mwamuna; ndipo mutu wa Khristu ndiye Mulungu.


Akazi inu, muzimvera amuna anu, monga kuyenera mwa Ambuye.


komatu (umo mokomera akazi akuvomereza kulemekeza Mulungu), mwa ntchito zabwino.


akhale odziletsa, odekha, ochita m'nyumba mwao, okoma, akumvera amuna a iwo okha, kuti mau a Mulungu angachitidwe mwano.


Momwemonso, akazi inu, mverani amuna anu a inu nokha; kuti, ngatinso ena samvera mau, akakodwe opanda mau mwa mayendedwe a akazi;


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa