1 Timoteyo 2:1 - Buku Lopatulika1 Ndidandaulira tsono, poyambayamba, kuti achitike mapembedzo, mapemphero, mapembedzero, mayamiko, chifukwa cha anthu onse; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20141 Ndidandaulira tsono, poyambayamba, kuti achitike mapembedzo, mapemphero, mapembedzero, mayamiko, chifukwa cha anthu onse; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa1 Tsono choyamba ndikukupemphani kuti pakhale mapemphero opempherera anthu onse. Mapemphero ake akhale opemba, opempha ndi othokoza Mulungu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero1 Tsono choyamba ndikukupemphani kuti mupempherere anthu onse. Mapemphero anu akhale opemba, opempha, opempherera ena ndi oyamika. Onani mutuwo |