1 Timoteyo 1:8 - Buku Lopatulika8 Koma mudziwa kuti lamulo ndi labwino, ngati munthu achita nalo monga mwa lamulo, Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20148 Koma mudziwa kuti lamulo ndi labwino, ngati munthu achita nalo monga mwa lamulo, Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa8 Tikudziŵa kuti Malamulo ngabwino, malinga nkuŵagwiritsa ntchito moyenera. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero8 Tikudziwa kuti Malamulo ndi abwino ngati munthu awagwiritsa ntchito bwino. Onani mutuwo |