1 Samueli 30:25 - Buku Lopatulika25 Ndipo kuyambira tsiku lija kufikira lero lomwe anaika ichi, chikhale lemba ndi chiweruzo pa Aisraele. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201425 Ndipo kuyambira tsiku lija kufikira lero lomwe anaika ichi, chikhale lemba ndi chiweruzo pa Aisraele. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa25 Tsono Davide adagamula kuti njira imeneyi ikhale lamulo lokhazikika pakati pa Aisraele, kuyambira tsiku limenelo mpaka pano. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero25 Choncho Davide anakhazikitsa ngati lamulo mʼchitidwe woterewu pakati pa Aisraeli kuyambira tsiku limenelo mpaka lero. Onani mutuwo |