1 Samueli 29:10 - Buku Lopatulika10 Chifukwa chake ulawirire m'mawa pamodzi ndi anyamata a mbuye wako amene anabwera nawe; ndipo mutauka m'mawa, mumuke kutacha. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201410 Chifukwa chake ulawirire m'mawa pamodzi ndi anyamata a mbuye wako amene anabwera nawe; ndipo mutauka m'mawa, mumuke kutacha. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa10 Tsono udzuke m'mamaŵa, pamodzi ndi anthu ako amene udabwera nawo, munyamuke kukangocha.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero10 Tsono udzuke mmamawa, pamodzi ndi ankhondo ako amene unabwera nawo, ndipo unyamuke kukangocha.” Onani mutuwo |