1 Samueli 25:37 - Buku Lopatulika37 Tsono m'mawa vinyo atamchokera Nabala, mkazi wake anamuuza zimenezi; ndipo mtima wake unamyuka m'kati mwake, iye nasanduka ngati mwala. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201437 Tsono m'mawa vinyo atamchokera Nabala, mkazi wake anamuuza zimenezi; ndipo mtima wake unamyuka m'kati mwake, iye nasanduka ngati mwala. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa37 M'maŵa mwake, m'maso mwa Nabala mutayera, mkazi wakeyo adamuuza zonse. Pomwepo Nabala mtima wake udaima, ndipo thupi lidangoti gwa ngati mwala. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero37 Tsono mmawa, mowa utamuchoka Nabala, mkazi wake anamuwuza zonse. Pomwepo mtima wake unaleka kugunda ndipo unawuma gwaa ngati mwala. Onani mutuwo |