1 Samueli 25:35 - Buku Lopatulika35 Chomwecho Davide analandira m'dzanja lake zimene iye anamtengera; nanena naye, Ukwere kwanu mumtendere; ona, ndamvera mau ako, ndavomereza nkhope yako. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201435 Chomwecho Davide analandira m'dzanja lake zimene iye anamtengera; nanena naye, Ukwere kwanu mumtendere; ona, ndamvera mau ako, ndavomereza nkhope yako. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa35 Motero Davide adalandira kwa mkaziyo zimene adaamtengera, namuuza kuti, “Pitani kunyumba kwanu ndi mtendere. Mau anu ndaŵamva ndipo zopempha ndavomera.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero35 Ndipo Davide analandira kwa mayiyo zimene anamutengera ndipo anati, “Pitani kwanu mu mtendere. Ine ndamva mawu anu ndipo ndavomera zimene mwapempha.” Onani mutuwo |