1 Samueli 23:15 - Buku Lopatulika15 Ndipo Davide anaona kuti Saulo adatuluka kudzafuna moyo wake; Davide nakhala m'chipululu cha Zifi m'nkhalango ku Horesi. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201415 Ndipo Davide anaona kuti Saulo adatuluka kudzafuna moyo wake; Davide nakhala m'chipululu cha Zifi m'nkhalango ku Horesi. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa15 Davide adaona kuti Saulo akumfunafuna kuti amuphe. Pa nthaŵiyo Davide anali ku chipululu cha Zifi ku Horesi. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero15 Davide anaona kuti Sauli akufunafuna kuti amuphe. Nthawiyi nʼkuti Davide ali mʼchipululu cha Zifi ku Horesi. Onani mutuwo |