1 Samueli 21:6 - Buku Lopatulika6 Chomwecho wansembeyo anampatsa mkate wopatulika, popeza panalibe mkate wina, koma mkate woonekera, umene adauchotsa pamaso pa Yehova, kuti akaike mkate wotentha tsiku lomwelo anachotsa winawo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20146 Chomwecho wansembeyo anampatsa mkate wopatulika, popeza panalibe mkate wina, koma mkate woonekera, umene adauchotsa pamaso pa Yehova, kuti akaike mkate wotentha tsiku lomwelo anachotsa winawo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa6 Apo wansembeyo adapereka buledi wachipembedzo kwa Davide, pakuti kunalibe buledi wina, koma buledi yekha woperekedwa kwa Chauta. Buledi wake ndi amene anali atamchotsa pamaso pa Chauta kuti akaikepo wina wamoto. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero6 Choncho wansembe uja anamupatsa buledi wachipembedzo popeza kunalibeko buledi wina aliyense koma yekhayo amene amaperekedwa kwa Yehova. Uyu ndi amene anachotsedwa tsiku limenelo kuti ayikepo wina wotentha. Onani mutuwo |