1 Samueli 20:33 - Buku Lopatulika33 Ndipo Saulo anamponyera mkondo kuti amgwaze; momwemo Yonatani anazindikira kuti atate wake anatsimikiza mtima kupha Davide. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201433 Ndipo Saulo anamponyera mkondo kuti amgwaze; momwemo Yonatani anazindikira kuti atate wake anatsimikiza mtima kupha Davide. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa33 Atamva zimenezi Saulo adamponyera mkondo Yonataniyo kuti amuphe. Pamenepo Yonatani adadziŵa kuti bambo wake watsimikizadi mtima kuti aphe Davide. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero33 Apo Sauli anamuponyera mkondo wake kuti amuphe. Tsono Yonatani anadziwa kuti abambo ake atsimikiza mtima kuti aphe Davide. Onani mutuwo |