1 Samueli 14:35 - Buku Lopatulika35 Ndipo Saulo anamangira Yehova guwa la nsembe; limenelo ndilo guwa loyamba iye anamangira Yehova. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201435 Ndipo Saulo anamangira Yehova guwa la nsembe; limenelo ndilo guwa loyamba iye anamangira Yehova. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa35 Tsono Saulo adamangira Chauta guwa. Limeneli linali guwa loyamba limene Sauloyo adamangira Chauta. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero35 Ndipo Sauli anamangira Yehova guwa. Ili linali guwa loyamba limene Sauli anamangira Yehova. Onani mutuwo |