1 Mbiri 9:9 - Buku Lopatulika9 ndi abale ao monga mwa mibadwo yao mazana asanu ndi anai mphambu makumi asanu kudza asanu ndi mmodzi. Onsewa ndiwo akulu a nyumba za makolo ao m'nyumba za makolo ao. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20149 ndi abale ao monga mwa mibadwo yao mazana asanu ndi anai mphambu makumi asanu kudza asanu ndi mmodzi. Onsewa ndiwo akulu a nyumba za makolo ao m'nyumba za makolo ao. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa9 Ndipo mabanja ao potsata mibadwo yao analipo 956. Onse amene alembedwa pamwambapaŵa anali atsogoleri a mabanja. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero9 Anthu ochokera ku Benjamini monga analembedwera mwa mibado yawo, analipo 956. Anthu onsewa anali atsogoleri a mabanja awo. Onani mutuwo |