Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




1 Mbiri 9:8 - Buku Lopatulika

8 ndi Ibineya mwana wa Yerohamu, ndi Ela mwana wa Uzi, mwana wa Mikiri, ndi Mesulamu mwana wa Sefatiya, mwana wa Reuwele, mwana wa Ibineya,

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

8 ndi Ibineya mwana wa Yerohamu, ndi Ela mwana wa Uzi, mwana wa Mikiri, ndi Mesulamu mwana wa Sefatiya, mwana wa Reuwele, mwana wa Ibineya,

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

8 Ibineya mwana wa Yerohamu, Ela mwana wa Uzi, mwana wa Mikiri ndiponso Mesulamu, mwana wa Sefatiya, mwana wa Reuwele, mwana wa Ibineya.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

8 Ibineya mwana wa Yerohamu; Ela mwana wa Uzi, mwana wa Mikiri; ndi Mesulamu mwana wa Sefatiya, mwana wa Reueli mwana wa Ibiniya.

Onani mutuwo Koperani




1 Mbiri 9:8
2 Mawu Ofanana  

Ndi a ana a Benjamini: Salu mwana wa Mesulamu, mwana wa Hodaviya, mwana wa Hasenuwa;


ndi abale ao monga mwa mibadwo yao mazana asanu ndi anai mphambu makumi asanu kudza asanu ndi mmodzi. Onsewa ndiwo akulu a nyumba za makolo ao m'nyumba za makolo ao.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa