1 Mbiri 9:7 - Buku Lopatulika7 Ndi a ana a Benjamini: Salu mwana wa Mesulamu, mwana wa Hodaviya, mwana wa Hasenuwa; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20147 Ndi a ana a Benjamini: Salu mwana wa Mesulamu, mwana wa Hodaviya, mwana wa Hasenuwa; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa7 A kwa Abenjamini anali aŵa: Salu, mwana wa Mesulamu, mwana wa Hodaviya, mwana wa Hasenuwa, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero7 A fuko la Benjamini: Salu mwana wa Mesulamu, mwana wa Hodaviya, mwana wa Hasenuya; Onani mutuwo |
Ndipo Ezara mlembi anaima pa chiunda cha mitengo adachimangira msonkhanowo; ndi pambali pake padaima Matitiya, ndi Sema, ndi Anaya, ndi Uriya, ndi Hilikiya, ndi Maaseiya, kudzanja lamanja lake; ndi kudzanja lamanzere Pedaya, ndi Misaele, ndi Malikiya, ndi Hasumu, ndi Hasibadana, Zekariya, ndi Mesulamu.