Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




1 Mbiri 9:6 - Buku Lopatulika

6 Ndi a ana a Zera: Yeuwele ndi abale ao mazana asanu ndi limodzi mphambu makumi asanu ndi anai.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

6 Ndi a ana a Zera: Yeuwele ndi abale ao mazana asanu ndi limodzi mphambu makumi asanu ndi anai.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

6 A kwa Azera anali aŵa: Yeuwele ndi achibale ao, onse pamodzi 690.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

6 A banja la Zera: Yeueli. Anthu ochokera ku Yuda analipo 690.

Onani mutuwo Koperani




1 Mbiri 9:6
7 Mawu Ofanana  

Ndipo pambuyo pake anabadwa mbale wake, amene anali ndi chingwe chofiira pamkono pake, dzina lake linatchedwa Zera.


Ndi ana aamuna a Yuda: Eri, ndi Onani, ndi Sela, ndi Perezi, ndi Zera; koma Eri ndi Onani anafa m'dziko la Kanani. Ndi ana aamuna a Perezi ndiwo Hezironi ndi Hamuli.


Ndi Tamara mpongozi wake anambalira Perezi ndi Zera. Ana aamuna onse a Yuda ndiwo asanu.


Ndi ana a Zera: Zimiri, ndi Etani, ndi Hemani, ndi Kalikoli, ndi Dara; onse pamodzi ndi asanu.


Ndipo a Asiloni: Asaya woyamba, ndi ana ake.


Ndi a ana a Benjamini: Salu mwana wa Mesulamu, mwana wa Hodaviya, mwana wa Hasenuwa;


Ndipo ana a Yuda monga mwa mabanja ao ndiwo: Sela, ndiye kholo la banja la Asela; Perezi, ndiye kholo la banja la Aperezi; Zera, ndiye kholo la banja la Azera.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa