Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




1 Mbiri 9:5 - Buku Lopatulika

5 Ndipo a Asiloni: Asaya woyamba, ndi ana ake.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

5 Ndipo a Asiloni: Asaya woyamba, ndi ana ake.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

5 A kwa Asiloni anali aŵa: Asaya mwana wachisamba pamodzi ndi ana ake.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

5 A banja la Siloni: Asaya mwana wake woyamba pamodzi ndi ana ake.

Onani mutuwo Koperani




1 Mbiri 9:5
4 Mawu Ofanana  

Utai mwana wa Amihudi, mwana wa Omuri, mwana wa Imuri, mwana wa Bani, wa ana a Perezi mwana wa Yuda.


Ndi a ana a Zera: Yeuwele ndi abale ao mazana asanu ndi limodzi mphambu makumi asanu ndi anai.


ndi Maaseiya mwana wa Baruki, mwana wa Kolihoze, mwana wa Hazaya, mwana wa Adaya, mwana wa Yoyaribu, mwana wa Zekariya, mwana wa Msiloni.


Ndipo ana a Yuda monga mwa mabanja ao ndiwo: Sela, ndiye kholo la banja la Asela; Perezi, ndiye kholo la banja la Aperezi; Zera, ndiye kholo la banja la Azera.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa