Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




1 Mbiri 9:3 - Buku Lopatulika

3 Ndipo mu Yerusalemu munakhala a ana a Yuda, ndi a ana a Benjamini, ndi a ana a Efuremu ndi Manase:

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

3 Ndipo m'Yerusalemu munakhala a ana a Yuda, ndi a ana a Benjamini, ndi a ana a Efuremu ndi Manase:

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

3 Anthu ena a ku Yuda, Benjamini, Efuremu ndi Manase amene ankakhala ku Yerusalemu anali motere:

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

3 Anthu a ku Yuda, Benjamini ndi Efereimu ndiponso Manase amene anakhala mu Yerusalemu anali awa:

Onani mutuwo Koperani




1 Mbiri 9:3
6 Mawu Ofanana  

Awa ndi akulu a nyumba za makolo mwa mibadwo yao, ndiwo akulu anakhala mu Yerusalemu awa.


Utai mwana wa Amihudi, mwana wa Omuri, mwana wa Imuri, mwana wa Bani, wa ana a Perezi mwana wa Yuda.


Ndipo akuwatsata iwo anadza ku Yerusalemu, ochokera m'mafuko onse a Israele, iwo akupereka mitima yao kufuna Yehova Mulungu wa Israele, kudzaphera Yehova Mulungu wa makolo ao nsembe.


Komatu ena a Asere ndi Manase ndi a Zebuloni anadzichepetsa, nadza ku Yerusalemu.


Ndipo akulu a anthu anakhala mu Yerusalemu; anthu otsala omwe anachita maere, kuti libwere limodzi la magawo khumi likhale mu Yerusalemu, mzinda wopatulika, ndi asanu ndi anai akhumi m'mizinda ina.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa