1 Mbiri 8:8 - Buku Lopatulika8 Ndipo Saharaimu anabala ana ku dziko la Mowabu, atachotsa akazi ake Husimu ndi Baara. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20148 Ndipo Saharaimu anabala ana ku dziko la Mowabu, atachotsa akazi ake Husimu ndi Baara. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa8 Saharaimu, atachotsa akazi ake Husimu ndi Baara, adakhala ndi ana m'dziko la Mowabu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero8 Saharaimu anabereka ana ku Mowabu atalekana ndi akazi ake, Husimu ndi Baara. Onani mutuwo |