1 Mbiri 8:7 - Buku Lopatulika7 natenga ndende Naamani, ndi Ahiya, ndi Gera, ndipo, anabala Uza, ndi Ahihudi. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20147 natenga ndende Naamani, ndi Ahiya, ndi Gera, ndipo, anabala Uza, ndi Ahihudi. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa7 Anawo anali Namani, Ahiya ndi Gera. Gerayo amene anali bambo wake wa Uza ndi Ahihudi, ndiye adatsogolera anthu osamutsidwawo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero7 Naamani, Ahiya ndi Gera, amene anawasamutsa ndipo anabereka Uza ndi Ahihudi. Onani mutuwo |