Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




1 Mbiri 8:6 - Buku Lopatulika

6 Ndi ana a Ehudi ndi awa: ndiwo akulu a nyumba za makolo ao a iwo okhala ku Geba, ndipo anawatenga ndende kunka ku Manahati,

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

6 Ndi ana a Ehudi ndi awa: ndiwo akulu a nyumba za makolo ao a iwo okhala ku Geba, ndipo anawatenga ndende kunka ku Manahati,

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

6 Ana a Ehudi amene anali atsogoleri a mabanja okhala ku Geba, adachotsedwa kwaoko ndipo adakakhala ku Manahati.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

6 Zidzukulu za Ehudi, zimene zinali atsogoleri a mabanja a amene amakhala ku Geba ndipo zinasamutsidwa kupita ku Manahati zinali izi:

Onani mutuwo Koperani




1 Mbiri 8:6
11 Mawu Ofanana  

Ndi ana aamuna a Benjamini: Bela ndi Bekere, ndi Asibele, ndi Gera, ndi Naamani, ndi Ehi ndi Rosi, Mupimu ndi Hupimu, ndi Aridi.


Ndi ana a Yerameele mwana woyamba wa Hezironi ndiwo: woyamba Ramu, ndi Buna, ndi Oreni, ndi Ozemu, ndi Ahiya.


Ndipo Sobala atate wa Kiriyati-Yearimu anali ndi ana: Harowe, ndi Hazi Amenuwoti.


Ana a Salima: Betelehemu, ndi Anetofa, Ataroti-Beti-Yowabu, ndi Hazi Amanahati, ndi Azori.


ndi ku fuko la Benjamini Geba ndi mabusa ake, ndi Alemeti ndi mabusa ake, ndi Anatoti ndi mabusa ake. Mizinda yao yonse mwa mabanja ao ndiyo mizinda khumi ndi itatu.


Ndi mwana wa Yediyaele: Bilihani; ndi ana a Bilihani: Yeusi, ndi Benjamini, ndi Ehudi, ndi Kenana, ndi Zetani, ndi Tarisisi, ndi Ahisahara.


ndi Gera, ndi Sefufani, ndi Huramu.


natenga ndende Naamani, ndi Ahiya, ndi Gera, ndipo, anabala Uza, ndi Ahihudi.


Ndipo motapira fuko la Benjamini, Gibiyoni ndi mabusa ake, Geba ndi mabusa ake,


Ndipo ana a Israele anaonjeza kuchita choipa pamaso pa Yehova, atafa Ehudi.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa