Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




1 Mbiri 8:5 - Buku Lopatulika

5 ndi Gera, ndi Sefufani, ndi Huramu.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

5 ndi Gera, ndi Sefufani, ndi Huramu.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

5 Gera, Sefufani ndiponso Huramu.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

5 Gera, Sefufani ndi Hiramu.

Onani mutuwo Koperani




1 Mbiri 8:5
5 Mawu Ofanana  

Supimu yemwe ndi Hupimu ana a Iri, ndi Husimu mwana wa Aheri.


ndi Abisuwa, ndi Naamani, ndi Ahowa,


Ndi ana a Ehudi ndi awa: ndiwo akulu a nyumba za makolo ao a iwo okhala ku Geba, ndipo anawatenga ndende kunka ku Manahati,


Sefufamu ndiye kholo la banja la Asefufamu; Hufamu, ndiye kholo la banja la Ahufamu.


Koma pamene ana a Israele anafuula kwa Yehova, Yehova anawaukitsira mpulumutsi, Ehudi mwana wa Gera, Mbenjamini, munthu wamanzere, ndipo ana a Israele anatumiza mtulo m'dzanja lake kwa Egiloni mfumu ya Mowabu.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa