Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




1 Mbiri 8:13 - Buku Lopatulika

13 ndi Beriya, ndi Sema; ndiwo akulu a nyumba za makolo a iwo okhala mu Ayaloni, amene anathawitsa okhala mu Gati;

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

13 ndi Beriya, ndi Sema; ndiwo akulu a nyumba za makolo a iwo okhala m'Ayaloni, amene anathawitsa okhala m'Gati;

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

13 Beriya ndi Sema anali atsogoleri a mabanja okhala ku mzinda wa Aiyaloni. Iwowo adathaŵitsa nzika za ku Gati.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

13 ndiponso Beriya ndi Sema, amene anali atsogoleri a mabanja a amene ankakhala ku Ayaloni ndipo anathamangitsa nzika za ku Gati.

Onani mutuwo Koperani




1 Mbiri 8:13
8 Mawu Ofanana  

Ndipo Sobala atate wa Kiriyati-Yearimu anali ndi ana: Harowe, ndi Hazi Amenuwoti.


ndi Penuwele atate wa Gedori, ndi Ezere atate wa Husa. Awa ndi ana a Huri woyamba wa Efurata atate wa Betelehemu.


Ndi ana a Elipaala: Eberi, ndi Misamu, ndi Semedi, amene anamanga Ono, ndi Lodi ndi midzi yake,


ndi Ahiyo, Sasaki, ndi Yeremoti,


Pomwepo Yoswa ananena kwa Yehova tsiku limene Yehova anapereka Aamori pamaso pa ana a Israele; ndipo anati pamaso pa Israele, Dzuwa iwe, linda, pa Gibiyoni, ndi Mwezi iwe, m'chigwa cha Ayaloni.


Panalibe Aanaki otsala m'dziko la ana a Israele; koma mu Gaza ndi mu Gati ndi mu Asidodi anatsalamo ena.


Saalabini, ndi Ayaloni ndi Itila;


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa