Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




1 Mbiri 8:12 - Buku Lopatulika

12 Ndi ana a Elipaala: Eberi, ndi Misamu, ndi Semedi, amene anamanga Ono, ndi Lodi ndi midzi yake,

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

12 Ndi ana a Elipaala: Eberi, ndi Misamu, ndi Semedi, amene anamanga Ono, ndi Lodi ndi milaga yake,

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

12 Ana a Elipaala naŵa: Ebere, Misamu ndi Semedi. Semedi ndiye adamanga mizinda ya Ono ndi Lodi pamodzi ndi midzi yake yomwe.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

12 Ana a Elipaala anali awa: Eberi, Misamu, Semedi (amene anamanga mizinda ya Ono ndi Lodi ndi midzi yake yozungulira)

Onani mutuwo Koperani




1 Mbiri 8:12
8 Mawu Ofanana  

Ndi Husimu anambalira Abitubu, ndi Elipaala.


ndi Beriya, ndi Sema; ndiwo akulu a nyumba za makolo a iwo okhala mu Ayaloni, amene anathawitsa okhala mu Gati;


Ana a Lodi, Hadidi, ndi Ono, mazana asanu ndi awiri mphambu makumi awiri kudza asanu.


Lodi, ndi Ono, chigwa cha amisiri.


anatumiza mau kwa ine Sanibalati ndi Gesemu, kuti, Tiyeni tikomane kumidzi ya ku Chigwa cha Ono; koma analingirira za kundichitira choipa.


Ana a Lodi, Hadidi, ndi Ono, mazana asanu ndi awiri mphambu makumi awiri kudza mmodzi.


Koma kunali, pakupita Petro ponseponse, anatsikiranso kwa oyera mtima akukhala ku Lida.


Ndipo anamuona iye onse akukhala ku Lida ndi ku Saroni, natembenukira kwa Ambuye amenewa.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa