1 Mbiri 8:10 - Buku Lopatulika10 ndi Yeuzi, ndi Sakiya, ndi Mirima. Awa ndi ana ake aakulu a nyumba za makolo ao. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201410 ndi Yeuzi, ndi Sakiya, ndi Mirima. Awa ndi ana ake akulu a nyumba za makolo ao. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa10 Yeuzi, Sakiya ndi Mirima. Ameneŵa ndiwo amene anali ana ake, atsogoleri a mabanja. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero10 Yeusi, Sakiya ndi Mirima. Awa ndiye ana ake, atsogoleri a mabanja awo. Onani mutuwo |