1 Mbiri 8:1 - Buku Lopatulika1 Ndipo Benjamini anabala Bela mwana wake woyamba, Asibele wachiwiri, ndi Ahara wachitatu, Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20141 Ndipo Benjamini anabala Bela mwana wake woyamba, Asibele wachiwiri, ndi Ahara wachitatu, Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa1 Benjamini adabereka Bela mwana wake wachisamba, Asibele mwana wake wachiŵiri, Ahara mwana wake wachitatu, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero1 Benjamini anabereka Bela mwana wake woyamba, wachiwiri Asibeli, wachitatu Ahara, Onani mutuwo |